Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Salimo 107:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Amasandutsa mitsinje kukhala chipululu,

      Ndiponso akasupe a madzi kukhala malo ouma.+

  • Yesaya 44:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Yesaya 50:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Ndiye nʼchifukwa chiyani nditabwera sindinapeze aliyense?

      Nʼchifukwa chiyani nditaitana palibe amene anayankha?+

      Kodi dzanja langa lafupika kwambiri moti silingathe kuwombola,

      Kapena kodi ine ndilibe mphamvu zopulumutsira?+

      Inetu ndimaumitsa nyanja pongoidzudzula chabe.+

      Mitsinje ndimaisandutsa chipululu.+

      Nsomba zake zimawola chifukwa chakuti mulibe madzi

      Ndipo zimafa chifukwa cha ludzu.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani