-
2 Mbiri 15:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Kwa nthawi yaitali, Aisiraeli anakhala opanda Mulungu woona, opanda wansembe woti aziwaphunzitsa ndiponso opanda malamulo.+
-
-
2 Mbiri 15:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Mtundu unkamenyana ndi mtundu wina ndiponso mzinda ndi mzinda wina, chifukwa Mulungu anawasiya kuti asokonezeke ndi mavuto osiyanasiyana.+
-