Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Yesaya 37:37, 38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Choncho Senakeribu mfumu ya Asuri anachoka nʼkubwerera kukakhala ku Nineve.+ 38 Pamene Senakeribu ankaweramira mulungu wake Nisiroki mʼkachisi, ana ake Adarameleki ndi Sarezere anamupha ndi lupanga+ nʼkuthawira kudziko la Ararati.+ Kenako mwana wake Esari-hadoni+ anakhala mfumu mʼmalo mwake.

  • Yesaya 45:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Sonkhanani pamodzi ndipo mubwere.

      Mubwere pamodzi, inu anthu amene mwapulumuka ku mitundu ya anthu.+

      Amene amanyamula zifaniziro zawo zogoba sadziwa chilichonse

      Ndipo amapemphera kwa mulungu woti sangawapulumutse.+

  • Yesaya 46:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Iwo amamunyamula pamapewa awo.+

      Amamutenga nʼkukamuika pamalo ake ndipo mulunguyo amangoima pomwepo.

      Sasuntha pamene amuikapo.+

      Anthuwo amamuitana mofuula, koma sayankha.

      Sangapulumutse munthu amene ali pamavuto.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani