Salimo 51:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Salimo 103:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Yesaya 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Yesaya 43:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ineyo ndi amene ndikufafaniza zolakwa zako*+ chifukwa cha dzina langa,+Ndipo machimo ako sindidzawakumbukira.+ Yeremiya 33:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndidzawayeretsa ku zolakwa zonse zimene anandichimwira+ ndipo ndidzawakhululukira zolakwa zawo zonse zimene anandichimwira nʼkuphwanya nazo malamulo anga.+ Machitidwe 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
25 Ineyo ndi amene ndikufafaniza zolakwa zako*+ chifukwa cha dzina langa,+Ndipo machimo ako sindidzawakumbukira.+
8 Ndidzawayeretsa ku zolakwa zonse zimene anandichimwira+ ndipo ndidzawakhululukira zolakwa zawo zonse zimene anandichimwira nʼkuphwanya nazo malamulo anga.+