Yesaya 55:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chifukwa mudzapita mukusangalala,+Ndipo adzakubweretsani kwanu mwamtendere.+ Mukadzafika, mapiri ndi zitunda zidzafuula mosangalala,+Ndipo mitengo yonse yakutchire idzawomba mʼmanja.+
12 Chifukwa mudzapita mukusangalala,+Ndipo adzakubweretsani kwanu mwamtendere.+ Mukadzafika, mapiri ndi zitunda zidzafuula mosangalala,+Ndipo mitengo yonse yakutchire idzawomba mʼmanja.+