Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Yesaya 59:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Ayi si choncho. Koma zolakwa zanu nʼzimene zakulekanitsani ndi Mulungu wanu.+

      Machimo anu ndi amene amuchititsa kuti akubisireni nkhope yake,

      Ndipo sakufuna kumva zimene mukunena.+

  • Yeremiya 3:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Anthu amafunsa kuti: “Ngati mwamuna wathetsa ukwati ndi mkazi wake, ndipo mkaziyo akachokadi nʼkukakwatiwa ndi mwamuna wina, kodi mwamunayo angabwererenso kwa mkaziyo?”

      Kodi dzikoli silaipitsidwa kale kwambiri?+

      Yehova wanena kuti: “Iwe wachita uhule ndi amuna ambirimbiri.+

      Ndiye kodi pano ukufuna ubwererenso kwa ine?

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani