Salimo 102:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndithudi inu mudzanyamuka nʼkusonyeza Ziyoni chifundo,+Chifukwa imeneyi ndi nthawi yoti mumusonyeze kukoma mtima kwanu.+Nthawi yoikidwiratu yakwana.+ Yesaya 66:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Yeremiya 31:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iwo adzabwera nʼkufuula mosangalala pamwamba pa phiri la Ziyoni.+Nkhope zawo zidzawala chifukwa cha ubwino wa* Yehova.Chifukwa cha mbewu, vinyo watsopano+ ndi mafuta,Ndiponso chifukwa cha ana a nkhosa ndi ana a ngʼombe.+ Iwo adzakhala ngati dimba lothiriridwa bwino+Ndipo sadzakhalanso ofooka.”+
13 Ndithudi inu mudzanyamuka nʼkusonyeza Ziyoni chifundo,+Chifukwa imeneyi ndi nthawi yoti mumusonyeze kukoma mtima kwanu.+Nthawi yoikidwiratu yakwana.+
12 Iwo adzabwera nʼkufuula mosangalala pamwamba pa phiri la Ziyoni.+Nkhope zawo zidzawala chifukwa cha ubwino wa* Yehova.Chifukwa cha mbewu, vinyo watsopano+ ndi mafuta,Ndiponso chifukwa cha ana a nkhosa ndi ana a ngʼombe.+ Iwo adzakhala ngati dimba lothiriridwa bwino+Ndipo sadzakhalanso ofooka.”+