-
Yesaya 50:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
50 Yehova wanena kuti:
“Kodi kalata yothetsera ukwati+ wa mayi anu amene ndinawathamangitsa ili kuti?
Kapena kodi ndakugulitsani kwa munthu uti amene ndinali naye ngongole?
-