Yesaya 58:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mukatero kuwala kwanu kudzaonekera ngati mʼbandakucha,+Ndipo mudzachira mofulumira kwambiri. Chilungamo chanu chizidzayenda patsogolo panu,Ndipo ulemerero wa Yehova uzidzalondera kumbuyo kwanu.+
8 Mukatero kuwala kwanu kudzaonekera ngati mʼbandakucha,+Ndipo mudzachira mofulumira kwambiri. Chilungamo chanu chizidzayenda patsogolo panu,Ndipo ulemerero wa Yehova uzidzalondera kumbuyo kwanu.+