Ekisodo 14:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Yesaya 52:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chifukwa simudzachoka mopanikizika,Ndipo simudzafunika kuthawa,Popeza Yehova azidzayenda patsogolo panu,+Ndipo Mulungu wa Isiraeli azidzalondera kumbuyo kwanu.+
12 Chifukwa simudzachoka mopanikizika,Ndipo simudzafunika kuthawa,Popeza Yehova azidzayenda patsogolo panu,+Ndipo Mulungu wa Isiraeli azidzalondera kumbuyo kwanu.+