-
Yesaya 1:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Imvani inu okhala kumwamba, ndipo tcherani khutu inu okhala padziko lapansi,+
Chifukwa Yehova wanena kuti:
-
-
Yesaya 31:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 “Aisiraeli inu, bwererani kwa Mulungu amene mwamupandukira mopanda manyazi.+
-
-
Yesaya 59:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Ife tachimwa ndipo tamukana Yehova.
Tabwerera mʼmbuyo nʼkumusiya Mulungu wathu.
-