Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Yesaya 30:12, 13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Choncho Woyera wa Isiraeli wanena kuti:

      “Chifukwa chakuti mwakana mawu awa,+

      Mukudalira katangale komanso chinyengo

      Ndipo mukukhulupirira zinthu zimenezi,+

      13 Cholakwa chanuchi chidzakhala ngati mpanda wogumuka kwa inu,

      Ngati mpanda wautali umene wapendekeka ndipo watsala pangʼono kugwa.

      Udzagwa mwadzidzidzi mʼkanthawi kochepa.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani