Yesaya 25:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Yeremiya 31:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iwo adzabwera nʼkufuula mosangalala pamwamba pa phiri la Ziyoni.+Nkhope zawo zidzawala chifukwa cha ubwino wa* Yehova.Chifukwa cha mbewu, vinyo watsopano+ ndi mafuta,Ndiponso chifukwa cha ana a nkhosa ndi ana a ngʼombe.+ Iwo adzakhala ngati dimba lothiriridwa bwino+Ndipo sadzakhalanso ofooka.”+
12 Iwo adzabwera nʼkufuula mosangalala pamwamba pa phiri la Ziyoni.+Nkhope zawo zidzawala chifukwa cha ubwino wa* Yehova.Chifukwa cha mbewu, vinyo watsopano+ ndi mafuta,Ndiponso chifukwa cha ana a nkhosa ndi ana a ngʼombe.+ Iwo adzakhala ngati dimba lothiriridwa bwino+Ndipo sadzakhalanso ofooka.”+