-
Yeremiya 48:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Mowabu wachititsidwa manyazi ndipo wagwidwa ndi mantha aakulu.
Lirani mofuula.
Lengezani ku Arinoni+ kuti Mowabu wawonongedwa.
-