-
Salimo 46:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Mitundu ya anthu inachita phokoso, maufumu anagonjetsedwa.
Iye analankhula mokweza mawu ndipo dziko lapansi linasungunuka.+
-
-
Salimo 68:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
68 Mulungu anyamuke, adani ake amwazike,
Ndipo amene amadana naye athawe pamaso pake.+
-
-
Yesaya 17:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Mitundu ya anthu idzachita phokoso ngati mkokomo wa madzi ambiri.
Iye adzawadzudzula ndipo iwo adzathawira kutali.
Adzathamangitsidwa ngati mankhusu* ouluzika ndi mphepo mʼmapiri
Ndiponso ngati udzu wouma wouluzika ndi mphepo yamkuntho.
-