Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Yesaya 63:1-3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 63 Kodi amene akuchokera ku Edomuyu+ ndi ndani,

      Amene akuchokera ku Bozira+ atavala zovala zowala zamitundu yosiyanasiyana,*

      Amene zovala zake ndi zaulemelero,

      Ndiponso amene akuyenda ndi mphamvu zake zochuluka?

      “Ndine, amene ndikulankhula mwachilungamo,

      Amene ndili ndi mphamvu zambiri zotha kupulumutsa.”

       2 Nʼchifukwa chiyani zovala zanu zili zofiira,

      Ndipo nʼchifukwa chiyani zovala zanu zikuoneka ngati za munthu woponda mphesa mʼchoponderamo mphesa?+

       3 “Moponderamo mphesa ndapondapondamo ndekha.

      Palibe munthu wochokera pakati pa mitundu ya anthu amene anali nane.

      Ndinapitiriza kupondaponda adani anga nditakwiya,

      Ndipo ndinkawapondaponda ndili ndi ukali.+

      Magazi awo anawazikira pazovala zanga,

      Ndipo ndadetsa zovala zanga zonse.

  • Obadiya 8, 9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Yehova akuti: “Kodi pa tsiku limenelo,

      Sindidzawononga anthu anzeru mu Edomu,+

      Komanso anthu ozindikira mʼdera lamapiri la Esau?

       9 Iwe Temani,+ asilikali ako adzachita mantha,+

      Chifukwa aliyense mʼdera lamapiri la Esau adzaphedwa.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani