2 Mafumu 24:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehoyakini mfumu ya Yuda anapita kwa mfumu ya Babulo+ pamodzi ndi mayi ake, atumiki ake, akalonga ake ndi nduna za panyumba yake+ ndipo mfumu ya Babuloyo inamutenga nʼkupita naye ku ukapolo mʼchaka cha 8 cha ufumu wake.+ Yeremiya 22:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 ‘Pali ine, Mulungu wamoyo,’ akutero Yehova, ‘ngakhale iwe Koniya*+ mwana wa Yehoyakimu,+ mfumu ya Yuda, utakhala mphete yodindira kudzanja langa lamanja, ndingakuvule!
12 Yehoyakini mfumu ya Yuda anapita kwa mfumu ya Babulo+ pamodzi ndi mayi ake, atumiki ake, akalonga ake ndi nduna za panyumba yake+ ndipo mfumu ya Babuloyo inamutenga nʼkupita naye ku ukapolo mʼchaka cha 8 cha ufumu wake.+
24 ‘Pali ine, Mulungu wamoyo,’ akutero Yehova, ‘ngakhale iwe Koniya*+ mwana wa Yehoyakimu,+ mfumu ya Yuda, utakhala mphete yodindira kudzanja langa lamanja, ndingakuvule!