Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Yeremiya 40:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Patapita nthawi, akuluakulu onse a asilikali amene anali mʼdziko lonselo limodzi ndi asilikali awo, anamva kuti mfumu ya Babulo yaika Gedaliya mwana wa Ahikamu kuti akhale wolamulira dzikolo. Anamvanso kuti yamuika kuti azilamulira amuna, akazi ndi ana ochokera pakati pa anthu osauka mʼdzikolo amene sanatengedwe kupita ku Babulo.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani