-
Yeremiya 21:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Anthu amene adzatsale mumzindawu adzafa ndi lupanga, njala ndiponso mliri. Koma aliyense amene adzatuluke nʼkupita kukadzipereka mʼmanja mwa Akasidi amene akuzungulirani, adzakhalabe ndi moyo. Iye adzapulumutsa moyo wake.”’+
-
-
Yeremiya 42:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Choncho dziwani ndithu kuti mudzafa ndi lupanga, njala ndi mliri mʼdziko limene mukulakalaka kupita kuti muzikakhalako.”+
-