-
Yeremiya 48:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Chifukwa chakuti mukudalira ntchito zanu ndi chuma chanu,
Inunso mudzagwidwa ndi adani.
Ndipo Kemosi+ adzatengedwa kupita ku ukapolo
Pamodzi ndi ansembe ake ndi akalonga ake.
-