Yeremiya 48:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Yehova wanena kuti: ‘Taonani! Mofanana ndi chiwombankhanga chimene chimatsika nʼkugwira chakudya chake,+Mdani adzatambasula mapiko ake nʼkugwira Mowabu.+ Yeremiya 49:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Chifukwa ine ndalumbira pa dzina langa kuti Bozira adzakhala chinthu chochititsa mantha,+ adzanyozedwa, adzawonongedwa ndi kutembereredwa ndipo mizinda yake yonse idzakhala mabwinja mpaka kalekale,” akutero Yehova.+
40 Yehova wanena kuti: ‘Taonani! Mofanana ndi chiwombankhanga chimene chimatsika nʼkugwira chakudya chake,+Mdani adzatambasula mapiko ake nʼkugwira Mowabu.+
13 “Chifukwa ine ndalumbira pa dzina langa kuti Bozira adzakhala chinthu chochititsa mantha,+ adzanyozedwa, adzawonongedwa ndi kutembereredwa ndipo mizinda yake yonse idzakhala mabwinja mpaka kalekale,” akutero Yehova.+