Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Yesaya 13:20, 21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 MʼBabulo simudzakhalanso anthu,

      Ndipo sadzakhalanso malo oti anthu nʼkukhalamo ku mibadwo yonse.+

      Kumeneko Mluya sadzakhomako tenti yake

      Ndipo abusa sadzagonekako ziweto zawo.

      21 Nyama zamʼchipululu zidzagona kumeneko.

      Nyumba zawo zidzadzaza ndi akadzidzi.

      Nthiwatiwa zizidzakhala kumeneko,+

      Ndipo mbuzi zakutchire* zizidzadumphadumpha kumeneko.

  • Yeremiya 51:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Babulo adzakhala milu yamiyala,+

      Malo obisalamo mimbulu,+

      Chinthu chochititsa mantha komanso chimene anthu azidzachiimbira mluzu

      Ndipo simudzapezeka munthu wokhalamo.+

  • Chivumbulutso 18:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani