Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Yeremiya 32:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Kenako ndinapereka makalata a pangano ogulira mundawo kwa Baruki+ mwana wa Neriya,+ mwana wa Maseya. Ndinapereka makalatawo pamaso pa Hanameli mwana wa mʼbale wawo wa bambo anga, pamaso pa mboni zimene zinasaina makalatawo ndi pamaso pa Ayuda onse amene anali mʼBwalo la Alonda.+

  • Yeremiya 36:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndiyeno Yeremiya anaitana Baruki+ mwana wa Neriya nʼkumuuza mawu onse amene Yehova anamuuza ndipo Baruki analemba mawuwo mumpukutu.+

  • Yeremiya 45:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 Awa ndi mawu amene mneneri Yeremiya anauza Baruki+ mwana wa Neriya pa nthawi imene Baruki ankalemba mʼbuku mawu amene Yeremiya+ ankamuuza, mʼchaka cha 4 cha ulamuliro wa Yehoyakimu+ mwana wa Yosiya, mfumu ya Yuda. Yeremiya anati:

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani