-
Yeremiya 12:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Chifukwa ngakhale abale ako enieni, anthu a mʼnyumba ya bambo ako,
Akuchitira zinthu zachinyengo.+
Iwo akunenera zinthu zoipa mofuula.
Usawakhulupirire,
Ngakhale atamalankhula zinthu zabwino kwa iwe.
-
-
Mika 7:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Musamakhulupirire anzanu.
Musamadalire mnzanu wapamtima.+
Muzisamala ndi zimene mumauza amene mumagona naye pafupi.
-