Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Yeremiya 6:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Onse ndi anthu ouma khosi kwambiri,+

      Amayenda uku ndi uku nʼkumanena miseche.+

      Iwo ali ngati kopa* ndi chitsulo,

      Onsewo ndi anthu achinyengo.

  • Ezekieli 22:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Mwa iwe muli anthu amiseche amene amafuna kukhetsa magazi.+ Mulinso anthu amene amadya chakudya choperekedwa nsembe kwa mafano mʼmapiri ndipo amachita khalidwe lonyansa pakati panu.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani