Yeremiya 49:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Ponena za Aamoni+ Yehova wanena kuti: “Kodi Isiraeli alibe ana aamuna? Kodi alibe wolandira cholowa? Nʼchifukwa chiyani Malikamu+ watenga Gadi+ kuti akhale cholowa chake? Ndipo nʼchifukwa chiyani anthu ake akukhala mʼmizinda ya Isiraeli?” Ezekieli 25:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Iwe mwana wa munthu, yangʼana kwa Aamoni+ ndipo ulosere zoipa zimene zidzawachitikire.+
49 Ponena za Aamoni+ Yehova wanena kuti: “Kodi Isiraeli alibe ana aamuna? Kodi alibe wolandira cholowa? Nʼchifukwa chiyani Malikamu+ watenga Gadi+ kuti akhale cholowa chake? Ndipo nʼchifukwa chiyani anthu ake akukhala mʼmizinda ya Isiraeli?”