Yesaya 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Uwu ndi uthenga wokhudza Mowabu:+ Chifukwa chakuti wawonongedwa usiku umodzi wokha,Ari+ wa ku Mowabu wakhalitsidwa chete. Chifukwa chakuti wawonongedwa usiku umodzi wokha,Kiri+ wa ku Mowabu wakhalitsidwa chete. Yeremiya 48:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Ponena za Mowabu,+ Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti: “Tsoka Nebo+ chifukwa wawonongedwa! Kiriyataimu+ wachititsidwa manyazi ndipo walandidwa. Malo othawirako otetezeka* achititsidwa manyazi ndipo awonongedwa.+
15 Uwu ndi uthenga wokhudza Mowabu:+ Chifukwa chakuti wawonongedwa usiku umodzi wokha,Ari+ wa ku Mowabu wakhalitsidwa chete. Chifukwa chakuti wawonongedwa usiku umodzi wokha,Kiri+ wa ku Mowabu wakhalitsidwa chete.
48 Ponena za Mowabu,+ Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti: “Tsoka Nebo+ chifukwa wawonongedwa! Kiriyataimu+ wachititsidwa manyazi ndipo walandidwa. Malo othawirako otetezeka* achititsidwa manyazi ndipo awonongedwa.+