Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Yeremiya 9:25, 26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Yehova wanena kuti, “Taona masiku akubwera ndipo ndidzaimba mlandu aliyense wodulidwa koma amene sanachite mdulidwe wa mtima wake.+ 26 Ndidzaimba mlandu Iguputo,+ Yuda,+ Edomu,+ Aamoni+ ndi Mowabu+ komanso onse odulira ndevu zawo zamʼmbali amene amakhala mʼchipululu.+ Chifukwa mitundu yonse ndi yosadulidwa ndipo anthu onse a mʼnyumba ya Isiraeli sanachite mdulidwe wa mitima yawo.”+

  • Ezekieli 25:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ndidzapereka chiweruzo mʼdziko la Mowabu+ ndipo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.’

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani