-
Yoswa 7:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Akanani ndi anthu onse a mʼdzikoli adzamva zimenezi, ndipo adzabwera nʼkufafaniza dzina lathu padziko lapansi. Ndiye mudzateteza bwanji dzina lanu lalikulu?”+
-
-
Salimo 25:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Chifukwa cha dzina lanu, inu Yehova,+
Mundikhululukire tchimo langa, ngakhale kuti ndi lalikulu.
-