-
Yesaya 49:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Amene akukuzunza ndidzawachititsa kuti adye mnofu wawo womwe,
Ndipo adzaledzera ndi magazi awo omwe ngati kuti amwa vinyo wotsekemera.
-
-
Yeremiya 50:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Choncho Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti: ‘Ine ndilanga mfumu ya Babulo komanso dziko lake ngati mmene ndinalangira mfumu ya Asuri.+
-