-
2 Mafumu 14:23, 24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Mʼchaka cha 15 cha Amaziya mwana wa Yehoasi mfumu ya Yuda, Yerobowamu+ mwana wa Yehoasi mfumu ya Isiraeli anakhala mfumu ku Samariya ndipo analamulira zaka 41. 24 Iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova. Sanasiye kuchita machimo onse amene Aisiraeli ankachita chifukwa cha Yerobowamu mwana wa Nebati.+
-