Deuteronomo 32:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Kubwezera ndi kwanga, chilangonso ndi changa.+Zimenezi zidzachitika pa nthawi yoikidwiratu phazi lawo likadzaterereka,+Chifukwa tsiku la tsoka lawo layandikira,Ndipo zowagwera zifika mofulumira.’ Deuteronomo 32:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Ndikanola lupanga langa lonyezimira,Nʼkukonzekeretsa dzanja langa kuti lipereke chiweruzo,+Ndidzabwezera adani anga,+Ndipo ndidzapereka chilango kwa amene amadana nane. Yesaya 59:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iye adzawapatsa mphoto chifukwa cha zimene achita:+ Adani ake adzawapatsa mkwiyo ndipo anthu otsutsana naye adzawapatsa chilango.+ Ndipo zilumba adzazipatsa chilango chogwirizana ndi zochita zawo.
35 Kubwezera ndi kwanga, chilangonso ndi changa.+Zimenezi zidzachitika pa nthawi yoikidwiratu phazi lawo likadzaterereka,+Chifukwa tsiku la tsoka lawo layandikira,Ndipo zowagwera zifika mofulumira.’
41 Ndikanola lupanga langa lonyezimira,Nʼkukonzekeretsa dzanja langa kuti lipereke chiweruzo,+Ndidzabwezera adani anga,+Ndipo ndidzapereka chilango kwa amene amadana nane.
18 Iye adzawapatsa mphoto chifukwa cha zimene achita:+ Adani ake adzawapatsa mkwiyo ndipo anthu otsutsana naye adzawapatsa chilango.+ Ndipo zilumba adzazipatsa chilango chogwirizana ndi zochita zawo.