Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Yesaya 34:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 “Chifukwa lupanga langa lidzakhala magazi okhaokha kumwambako.+

      Lupangalo lidzatsikira pa Edomu kuti lipereke chiweruzo,+

      Lidzatsikira pa anthu amene ndikufuna kuwawononga.

  • Obadiya 18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 A mʼbanja la Yakobo adzakhala ngati moto,

      A mʼbanja la Yosefe adzakhala ngati malawi a moto,

      Ndipo a mʼbanja la Esau adzakhala ngati mapesi.

      Moto wawo udzayatsa ndi kunyeketsa mapesiwo,

      Ndipo palibe aliyense wa mʼbanja la Esau amene adzapulumuke,+

      Chifukwa Yehova ndi amene wanena.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani