-
Salimo 137:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Inu Yehova, kumbukirani
Zimene Aedomu ananena pa tsiku limene Yerusalemu anawonongedwa.
Iwo anati: “Gwetsani mzindawo! Ugwetseni mpaka pamaziko ake!”+
-
-
Yeremiya 49:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Ponena za Edomu, Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti:
“Kodi nzeru zinatha ku Temani?+
Kodi anthu ozindikira sakuperekanso malangizo anzeru?
Kodi nzeru zawo zinawola?
-