-
Yesaya 50:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Msana wanga ndinaupereka kwa anthu amene ankandimenya
Ndipo masaya anga ndinawapereka kwa anthu amene ankandizula ndevu.
Sindinabise nkhope yanga kuti asaichitire zinthu zochititsa manyazi komanso kuti asailavulire.+
-
-
Yesaya 53:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Iye anaponderezedwa ndipo anatengedwa popanda kuweruzidwa mwachilungamo.
Ndi ndani amene anaganizira tsatanetsatane wa mʼbadwo wa makolo ake?*
-