DEUTERONOMO
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
-  1  - 
- Kuchoka paphiri la Horebe (1-8) 
- Anasankha atsogoleri komanso oweruza (9-18) 
- Anthu sanamvere ku Kadesi-barinea (19-46) 
 
-  2  
-  3  - 
- Anagonjetsa Mfumu Ogi ya ku Basana (1-7) 
- Malire a dziko kumʼmawa kwa mtsinje wa Yorodano (8-20) 
- Yoswa anauzidwa kuti asachite mantha (21, 22) 
- Mose sadzalowa mʼdziko (23-29) 
 
-  4  - 
- Anawalimbikitsa kuti akhale omvera (1-14) 
- Yehova amafuna kuti anthu azidzipereka kwa iye yekha (15-31) 
- Palibe Mulungu wina kupatulapo Yehova (32-40) 
- Mizinda yothawirako kumʼmawa kwa Yorodano (41-43) 
- Anawapatsa Chilamulo (44-49) 
 
-  5  - 
- Yehova anachita pangano ku Horebe (1-5) 
- Anabwereza kuwauza Malamulo Khumi (6-22) 
- Anthu anachita mantha paphiri la Sinai (23-33) 
 
-  6  - 
- Muzikonda Yehova ndi mtima wanu wonse (1-9) 
- Musaiwale Yehova (10-15) 
- Musamamuyese Yehova (16-19) 
- Mudzafotokozere mʼbadwo wotsatira (20-25) 
 
-  7  - 
- Mitundu 7 yoyenera kuwonongedwa (1-6) 
- Chifukwa chimene anasankhira Aisiraeli (7-11) 
- Kumvera kumabweretsa madalitso (12-26) 
 
-  8  
-  9  
- 10  
- 11  - 
- Mwaona mphamvu za Yehova (1-7) 
- Dziko Lolonjezedwa (8-12) 
- Madalitso amene adzapeze chifukwa chomvera (13-17) 
- Muzisunga mawu a Mulungu mʼmitima yanu (18-25) 
- “Dalitso ndi temberero” (26-32) 
 
- 12  - 
- Muzilambira pamalo amene Mulungu anasankha (1-14) 
- Analoledwa kudya nyama koma osati magazi (15-28) 
- Musagwidwe mʼmisampha ya milungu ina (29-32) 
 
- 13  
- 14  - 
- Zinthu zosayenera kuchita polira maliro (1, 2) 
- Zakudya zodetsedwa komanso zosadetsedwa (3-21) 
- Chakhumi choperekedwa kwa Yehova (22-29) 
 
- 15  - 
- Ankakhululukira angongole chaka cha 7 chilichonse (1-6) 
- Kuthandiza osauka (7-11) 
- Akapolo ankamasulidwa chaka cha 7 chilichonse (12-18) 
- Nyama zoyamba kubadwa zinali zopatulika (19-23) 
 
- 16  - 
- Pasika; Chikondwerero cha Mikate Yopanda Zofufumitsa (1-8) 
- Chikondwerero cha Masabata (9-12) 
- Chikondwerero cha Misasa (13-17) 
- Kusankha oweruza (18-20) 
- Zinthu zosayenera kuzilambira (21, 22) 
 
- 17  - 
- Nsembe zizikhala zopanda chilema (1) 
- Zoyenera kuchita ndi ampatuko (2-7) 
- Milandu yovuta kuweruza (8-13) 
- Malangizo oti mafumu azidzatsatira (14-20) 
 
- 18  - 
- Zimene ansembe ndi Alevi ankayenera kulandira (1-8) 
- Anawaletsa kuchita zamizimu (9-14) 
- Mneneri ngati Mose (15-19) 
- Mmene tingadziwire aneneri abodza (20-22) 
 
- 19  - 
- Mlandu wa magazi komanso mizinda yothawirako (1-13) 
- Zizindikiro za malire sizinkafunika kusunthidwa (14) 
- Anthu operekera umboni mukhoti (15-21) 
 
- 20  
- 21  - 
- Ngati wopha munthu sakudziwika (1-9) 
- Kukwatira akazi ogwidwa kunkhondo (10-14) 
- Ufulu wa mwana woyamba kubadwa (15-17) 
- Mwana wosamvera (18-21) 
- Munthu wopachikidwa pamtengo ndi wotembereredwa (22, 23) 
 
- 22  - 
- Kulemekeza ziweto za anthu ena (1-4) 
- Kuvala zovala zachimuna kapena zachikazi (5) 
- Kuchitira chifundo ziweto (6, 7) 
- Kampanda kapadenga la nyumba (8) 
- Zinthu zosayenera kuphatikizidwa (9-11) 
- Ulusi wa mʼmphepete mwa zovala (12) 
- Malamulo a milandu yokhudza kugonana (13-30) 
 
- 23  - 
- Anthu osayenera kulowa mumpingo wa Mulungu (1-8) 
- Ukhondo mumsasa (9-14) 
- Kapolo amene wathawa kwa mbuye wake (15, 16) 
- Uhule unaletsedwa (17, 18) 
- Chiwongoladzanja komanso malonjezo (19-23) 
- Zimene anthu ongodutsa ankaloledwa kudya (24, 25) 
 
- 24  - 
- Ukwati komanso kutha kwa ukwati (1-5) 
- Kulemekeza moyo (6-9) 
- Kuganizira osauka (10-18) 
- Malamulo okhudza kukunkha (19-22) 
 
- 25  - 
- Malamulo okhudza kukwapula munthu (1-3) 
- Ngʼombe imene ikupuntha mbewu musamaimange pakamwa (4) 
- Ukwati wapachilamu (5-10) 
- Kugwira malo osayenera pandewu (11, 12) 
- Muyezo woyenera woyezera kulemera komanso kuchuluka kwa zinthu (13-16) 
- Aamaleki ayenera kuwonongedwa (17-19) 
 
- 26  - 
- Kupereka zipatso zoyambirira (1-11) 
- Chakhumi chachiwiri (12-15) 
- Aisiraeli anali chuma chapadera kwa Yehova (16-19) 
 
- 27  - 
- Akalembe Chilamulo pamiyala (1-10) 
- Paphiri la Ebala ndi paphiri la Gerizimu (11-14) 
- Anatchulanso matemberero (15-26) 
 
- 28  
- 29  
- 30  - 
- Kubwerera kwa Yehova (1-10) 
- Malamulo a Yehova si ovuta kwambiri (11-14) 
- Kusankha moyo kapena imfa (15-20) 
 
- 31  - 
- Mose anali atatsala pangʼono kumwalira (1-8) 
- Kuwerenga Chilamulo pamaso pa anthu (9-13) 
- Yoswa anamuika kuti akhale mtsogoleri (14, 15) 
- Ananeneratu kuti Aisiraeli adzapandukira Mulungu (16-30) 
 
- 32  
- 33  
- 34