Limbitsani Chikhulupiriro Chanu!
M’MAWA
- 9:40 Kumvetsera Nyimbo 
- 9:50 Nyimbo Na. 119 ndi Pemphero 
- 10:00 N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kulimbitsa Chikhulupiriro Chathu Panopa? 
- 10:15 Kodi Mumaona “Wosaonekayo”? 
- 10:30 “Munthu Amakhala ndi Chikhulupiriro Chifukwa cha Zimene Wamva” 
- 10:55 Nyimbo Na. 104 ndi Zilengezo 
- 11:05 “Makhalidwe Amene Mzimu Woyera Umatulutsa Ndiwo . . . Chikhulupiriro” 
- 11:35 Kudzipereka Ndiponso Kubatizidwa 
- 12:05 Nyimbo Na. 50 
MASANA
- 1:20 Kumvetsera Nyimbo 
- 1:30 Nyimbo Na. 3 
- 1:35 Zochitika pa Moyo Wachikhristu 
- 1:45 Phunziro Lachidule la Nsanja ya Olonda 
- 2:15 Nkhani Yosiyirana: Muzithandiza Ena Kukhala ndi Chikhulupiriro Cholimba - • Muzithandiza Ana Anu 
- • Muzithandiza Wophunzira Baibulo 
- • Muzithandiza Akhristu Anzanu 
 
- 3:00 Nyimbo Na. 38 ndi Zilengezo 
- 3:10 Tiziyang’anitsitsa “Mtumiki Wamkulu ndi Wokwaniritsa Chikhulupiriro Chathu” 
- 3:55 Nyimbo Na. 126 ndi Pemphero