Mupeze Mayankho a Mafunso Awa:
- 1. Kodi chidzachitike n’chiyani tikamasonyeza chikhulupiriro? (Yoh. 3:16) 
- 2. Kodi tingatsanzire bwanji chikhulupiriro cha Isaki ndi Rabeka, Esitere komanso Timoteyo? (Mlal. 4:11, 12; Sal. 119:46; 2 Tim. 1:5) 
- 3. N’chiyani chingatithandize kuti tizipitirizabe kulalikira ngakhale tikumane ndi mavuto? (2 Akor. 4:13) 
- 4. Kodi tingatani kuti ‘tiziyenda mwachikhulupiriro’ tsiku lililonse? (2 Akor. 5:7) 
- 5. Kodi tingatani kuti Yehova azitidziwa? (2 Tim. 2:19; Yak. 4:6; 2 Akor. 13:5) 
© 2021 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
CA-copgm22-MSL