Khalani ndi ‘Chikhulupiriro’
M’MAWA
- 9:30 Kumvetsera Nyimbo 
- 9:40 Nyimbo Na. 118 ndi Pemphero 
- 9:50 Mmene Tingasonyezere Kuti ‘Timakhulupirira’ Ndiponso Chifukwa Chake 
- 10:05 Nkhani Yosiyirana: Muzitsanzira Anthu Amene Anasonyeza Chikhulupiriro - • Isaki ndi Rabeka 
- • Esitere 
- • Timoteyo 
 
- 11:05 Nyimbo Na. 60 ndi Zilengezo 
- 11:15 ‘Tili ndi Chikhulupiriro, Chotero Timalankhula’ 
- 11:30 Kudzipereka Ndiponso Kubatizidwa 
- 12:00 Nyimbo Na. 52 
MASANA
- 1:10 Kumvetsera Nyimbo 
- 1:20 Nyimbo Na. 9 ndi Pemphero 
- 1:30 Nkhani ya Baibulo ya Onse: Muzikhulupirira Mulungu “Amene Sanganame” 
- 2:00 Phunziro Lachidule la Nsanja ya Olonda 
- 2:30 Nyimbo Na. 54 ndi Zilengezo 
- 2:40 Nkhani Yosiyirana: ‘Muziyenda mwa Chikhulupiriro’ Tsiku Lililonse - • “Musamade Nkhawa” 
- • “Muzigwiritsa Ntchito Bwino Nthawi Yanu” 
- • Musamakhale “Mbali ya Dziko” 
 
- 3:40 “Yehova Amadziwa Anthu Ake” 
- 4:15 Nyimbo Na. 7 ndi Pemphero