October 23-29
HOSEYA 8-14
Nyimbo Na. 153 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Muzipereka Zinthu Zabwino Kwambiri kwa Yehova”: (10 min.)
Hos. 14:2—Yehova amayamikira kwambiri nsembe zimene timamupatsa zomwe ndi “mawu apakamwa pathu” (w07 4/1 20 ¶2)
Hos. 14:4—Yehova amakonda anthu amene amachita zonse zomwe angathe pomutumikira, amawakhululukira machimo, komanso amawaona ngati anzake (w11 2/15 16 ¶15)
Hos. 14:9—Tikamayenda m’njira za Yehova timapindula kwambiri (jd 87 ¶11)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Hos. 10:12—Kodi tiyenera kuchita chiyani kuti ‘tikolole zipatso za kukoma mtima kosatha’ kwa Yehova? (w05 11/15 28 ¶7)
Hos. 11:1—Kodi mawu a mu vesili anakwaniritsidwa bwanji pa Yesu? (w11 8/15 10 ¶10)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Hos. 8:1-14
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) T-35
Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) T-35—Pitirizani kukambirana zokhudza kapepala kamene munamupatsa pa ulendo woyamba. Sonyezani mmene tingayankhire ngati mwininyumba akutsutsa mfundo inayake.
Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) lv 152 ¶13-14—Sonyezani mmene tingafikire pamtima wophunzira wathu.
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Muzitumikira Yehova Nthawi Zonse”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onetsani vidiyo yakuti Muzigwiritsa Ntchito Luso Lanu Kutumikira Yehova.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 9 ¶1-9, komanso tsamba 89
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 63 ndi Pemphero