Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb20.10 6
  • Makhalidwe Abwino Kwambiri a Yehova

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Makhalidwe Abwino Kwambiri a Yehova
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Timapindula Bwanji ndi Chikondi Chokhulupirika cha Yehova?
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2021
  • Chikondi Sichitha
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • Kodi Mumasangalala ndi Chikondi Chokhulupirika Ngati Mmene Yehova Amachitira?
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
  • Kodi Yehova Ndi Wotani?
    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale—Kuphunzira Baibulo Mokambirana
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20.10 6

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EKISODO 33-34

Makhalidwe Abwino Kwambiri a Yehova

34:5-7

Mose ankadziwa bwino kwambiri makhalidwe a Yehova ndipo zimenezi zinkamuthandiza kuchita zinthu moleza mtima ndi Aisiraeli. Ifenso tikadziwa bwino makhalidwe a Yehova tikhoza kumachita zinthu mwachifundo ndi Akhristu anzathu.

  • “Wachifundo ndi wachisomo”: Yehova amasamalira anthu ake mwachikondi kwambiri komanso amawadera nkhawa ngati mmene makolo amachitira ndi ana awo

  • “Wosakwiya msanga”: Yehova amalezera mtima atumiki ake. Iye amawamvetsa akalakwitsa zinthu ndipo amawapatsa nthawi kuti asinthe

  • “Wodzaza ndi kukoma mtima kosatha”: Chikondi cha Yehova ndi chokhulupirika moti adzakonda anthu ake mpaka kalekale

A Mboni za Yehova akutsanzira makhalidwe a Yehova. 1. Akulu awiri apita kukachezera banja kunyumba kwawo ndipo akuwalimbikitsa pogwiritsa ntchito mfundo za m’Baibulo. 2. Mlongo akulimbikitsa mlongo wina amene akulira.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndingatsanzire bwanji chifundo cha Yehova?’

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani