Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • mwb25.03 6
  • April 7-13

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • April 7-13
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Kabuku ka Msonkhano—2025
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Kabuku ka Msonkhano—2025
mwb25.03 6

APRIL 7-13

MIYAMBO 8

Nyimbo Na. 89 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yesu akuphunzitsa gulu la anthu panja.

1. Muzimvetsera Nzeru Yomwe Ikulankhula Ngati Munthu

(10 min.)

Yesu, yemwe akutchulidwa kuti “nzeru” m’buku la Miyambo, anali “woyamba kulengedwa ndi Yehova” (Miy 8:1, 4, 22; cf 131 ¶7)

Yesu anakhala ndi nzeru kwambiri komanso anayamba kukonda kwambiri Atate wake chifukwa chokhala nthawi yaitali pambali pa Yehova n’kumagwira nawo ntchito yolenga (Miy 8:30, 31; cf 131-132 ¶8-9)

Tikamamvetsera nzeru za Yesu m’pamene zimatithandiza (Miy 8:32, 35; w09 4/15 31 ¶14)

2. Mfundo Zothandiza

(10 min.)

  • Miy 8:1-3—Kodi nzeru imangokhalira “kufuula mokweza” m’njira yotani? (w22.10 43:1-2)

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

3. Kuwerenga Baibulo

(4 min.) Miy 8:22-31 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

4. Ulendo Wobwereza

(4 min.) KULALIKIRA MWAMWAYI. Yankhani mafunso amene munthu yemwe akuganiza zodzapezeka pa Chikumbutso ali nawo okhudza zomwe zimachitika pamwambowu. (lmd phunziro 9 mfundo 3)

5. Ulendo Woyamba

(3 min.) KULALIKIRA MWAMWAYI. Landirani munthu amene wabwera ku Chikumbutso atapeza kapepala komuitanira ku mwambowu pakhomo pake, ndipo muyankhe mafunso amene angakhale nawo pambuyo pamwambowu. (lmd phunziro 3 mfundo 5)

6. Kufotokoza Zimene Mumakhulupirira

(5 min.) Nkhani. ijwbq 160—Mutu: N’chifukwa Chiyani Baibulo Limati Yesu Ndi Mwana wa Mulungu? (th phunziro 1)

MOYO WATHU WA CHIKHRISTU

Nyimbo Na. 105

7. Zofunika Pampingo

(15 min.)

8. Phunziro la Baibulo la Mpingo

(30 min.) bt 21:14-22

Mawu Omaliza (3 min.) | Nyimbo Na. 103 ndi Pemphero

    Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
    • tumizirani
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • zachinsinsi
    • JW.ORG
    • Lowani
    tumizirani