MALIKO
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
-  1  - 
- Yohane Mʼbatizi ankalalikira (1-8) 
- Kubatizidwa kwa Yesu (9-11) 
- Yesu anayesedwa ndi Satana (12, 13) 
- Yesu anayamba kulalikira ku Galileya (14, 15) 
- Anasankha ophunzira oyambirira (16-20) 
- Anatulutsa mzimu wonyansa (21-28) 
- Yesu anachiritsa anthu ambiri ku Kaperenao (29-34) 
- Anapemphera kumalo opanda anthu (35-39) 
- Munthu wakhate anachiritsidwa (40-45) 
 
-  2  - 
- Yesu anachiritsa munthu wakufa ziwalo (1-12) 
- Yesu anaitana Levi (13-17) 
- Funso lokhudza kusala kudya (18-22) 
- Yesu ndi ‘Mbuye wa Sabata’ (23-28) 
 
-  3  - 
- Munthu wolumala dzanja anachiritsidwa (1-6) 
- Chigulu cha anthu chinali mʼmbali mwa nyanja (7-12) 
- Atumwi 12 (13-19) 
- Kunyoza mzimu woyera (20-30) 
- Mayi komanso azichimwene ake a Yesu (31-35) 
 
-  4  
-  5  
-  6  - 
- Yesu anakanidwa mʼdera lakwawo (1-6) 
- Atumwi 12 anapatsidwa malangizo okhudza utumiki (7-13) 
- Imfa ya Yohane Mʼbatizi (14-29) 
- Yesu anadyetsa anthu 5,000 (30-44) 
- Yesu anayenda pamadzi (45-52) 
- Anachiritsa anthu ku Genesareti (53-56) 
 
-  7  - 
- Anadzudzula miyambo ya anthu (1-13) 
- Zinthu zimene zimaipitsa munthu zimachokera mumtima (14-23) 
- Chikhulupiriro cha mayi wa Chisurofoinike (24-30) 
- Munthu amene anali ndi vuto losamva anachiritsidwa (31-37) 
 
-  8  - 
- Yesu anadyetsa anthu 4,000 (1-9) 
- Anapempha chizindikiro (10-13) 
- Zofufumitsa za Afarisi ndi Herode (14-21) 
- Munthu wavuto losaona anachiritsidwa ku Betsaida (22-26) 
- Petulo anazindikira kuti Yesu ndi Khristu (27-30) 
- Yesu ananeneratu za imfa yake (31-33) 
- Chizindikiro cha wophunzira weniweni (34-38) 
 
-  9  - 
- Yesu anasintha maonekedwe ake (1-13) 
- Mnyamata wogwidwa ndi chiwanda anachiritsidwa (14-29) 
- Yesu ananeneratu kachiwiri za imfa yake (30-32) 
- Ophunzira anakangana kuti wamkulu ndi ndani (33-37) 
- Aliyense amene sakulimbana nafe ali kumbali yathu (38-41) 
- Zopunthwitsa (42-48) 
- “Khalani ndi mchere mwa inu nokha” (49, 50) 
 
- 10  - 
- Ukwati komanso kutha kwa banja (1-12) 
- Yesu anadalitsa ana (13-16) 
- Funso la munthu wachuma (17-25) 
- Zinthu zimene tikuyenera kudzimana chifukwa cha Ufumu (26-31) 
- Yesu ananeneratunso za imfa yake (32-34) 
- Pempho la Yakobo ndi Yohane (35-45) 
- Batimeyu amene anali ndi vuto losaona anachiritsidwa (46-52) 
 
- 11  - 
- Yesu analowa mumzinda mwaulemerero (1-11) 
- Anatemberera mtengo wamkuyu (12-14) 
- Yesu anayeretsa kachisi (15-18) 
- Zimene tikuphunzira pa mtengo wamkuyu umene unafota (19-26) 
- Anatsutsa ulamuliro wa Yesu (27-33) 
 
- 12  - 
- Fanizo la alimi amene anapha anthu (1-12) 
- Mulungu komanso Kaisara (13-17) 
- Funso lokhudza kuuka kwa akufa (18-27) 
- Malamulo awiri aakulu kwambiri (28-34) 
- Kodi Khristu ndi mwana wa Davide? (35-37a) 
- Anawachenjeza kuti asamale ndi alembi (37b-40) 
- Timakobidi tiwiri ta mayi wamasiye wosauka (41-44) 
 
- 13  
- 14  - 
- Ansembe anakonza zoti aphe Yesu (1, 2) 
- Anathira Yesu mafuta onunkhira kwambiri (3-9) 
- Yudasi anapereka Yesu (10, 11) 
- Pasika womaliza (12-21) 
- Anayambitsa Mwambo wa Chakudya Chamadzulo cha Ambuye (22-26) 
- Ananeneratu zoti Petulo adzamukana (27-31) 
- Yesu anapemphera ku Getsemane (32-42) 
- Yesu anagwidwa (43-52) 
- Anaimbidwa mlandu Mʼkhoti Lalikulu la Ayuda (53-65) 
- Petulo anakana Yesu (66-72) 
 
- 15  - 
- Yesu anakaonekera pamaso pa Pilato (1-15) 
- Ananyozedwa pagulu (16-20) 
- Anamukhomerera pamtengo ku Gologota (21-32) 
- Imfa ya Yesu (33-41) 
- Kuikidwa mʼmanda kwa Yesu (42-47) 
 
- 16