Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 15
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Machitidwe 15:1

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aga 2:12
  • +Aga 5:2
  • +Ge 17:10; Eks 12:48; Le 12:3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 101-102

    Nsanja ya Olonda,

    4/15/1998, tsa. 22

    5/15/1995, ptsa. 11-12

    6/15/1990, ptsa. 12-13

    2/15/1989, tsa. 19

Machitidwe 15:2

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 11:30; 16:4; Aga 2:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 102-104

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 54

    Nsanja ya Olonda,

    5/15/1997, tsa. 16

    5/15/1995, ptsa. 11-12

    2/15/1989, tsa. 19

    8/1/1987, tsa. 12

Machitidwe 15:3

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 15:24; 1Ak 16:6
  • +Mac 13:4; 14:27
  • +Mac 11:18

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 104-105

Machitidwe 15:4

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 21:17
  • +Mac 21:19

Machitidwe 15:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 11:2
  • +Eks 12:48

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 105, 107

Machitidwe 15:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Miy 13:10; 15:22

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 105-106

Machitidwe 15:7

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mko 9:16; Mac 15:2
  • +Mac 10:34; 11:17

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 106

    Nsanja ya Olonda,

    6/15/1990, tsa. 13

Machitidwe 15:8

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Mb 28:9; Yer 11:20; Mac 1:24
  • +Mac 10:44; 11:15

Machitidwe 15:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aga 3:28
  • +Aga 2:16; 1Pe 1:22

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 106

Machitidwe 15:10

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aga 5:1
  • +Aga 3:10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 106

    Nsanja ya Olonda,

    6/15/1990, tsa. 13

Machitidwe 15:11

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 53:11; Yoh 1:17; Aga 2:16
  • +Mt 20:28

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 106

    Nsanja ya Olonda,

    6/15/1990, tsa. 13

Machitidwe 15:12

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 15:19

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 106

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 54

Machitidwe 15:13

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 12:17

Machitidwe 15:14

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 11:13; 2Pe 1:1
  • +Yes 55:5; 1Pe 2:9

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 108-109

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    10/2021, ptsa. 20-21

    Gulu, tsa. 162

    Nsanja ya Olonda,

    12/15/2014, tsa. 16

    11/15/2014, ptsa. 24-25

    3/15/2013, ptsa. 27-28

    6/15/1990, tsa. 13

Machitidwe 15:15

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 108-109

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 54

Machitidwe 15:16

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Amo 9:11

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 109

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/2013, ptsa. 8-9

    6/15/1990, tsa. 13

Machitidwe 15:17

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Amo 9:12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 109

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/2012, tsa. 5

Machitidwe 15:18

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 45:21

Machitidwe 15:19

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 15:10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 109-111

Machitidwe 15:20

Mawu a M'munsi

  • *

    Onani Zakumapeto 7.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Ge 35:2; Eks 20:3; Eze 20:30; 1Ak 8:7; 10:14
  • +1Ak 6:9; Akl 3:5; 1At 4:3
  • +Le 17:13
  • +Ge 9:4; Le 3:17; 7:26; 17:10; 19:26; De 12:23; 15:23; 1Sa 14:32

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Galamukani!,

    11/8/1990, tsa. 15

Machitidwe 15:21

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 13:15; 2Ak 3:15

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 109, 111

    Nsanja ya Olonda,

    5/1/1995, tsa. 11

    6/15/1990, tsa. 13

Machitidwe 15:22

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 1:23

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 113

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/1999, ptsa. 26-27

Machitidwe 15:23

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 11:26
  • +Aga 1:21

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2000, tsa. 26

Machitidwe 15:24

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 15:1
  • +Aga 2:4; Tit 1:10

Machitidwe 15:25

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 1:14
  • +2Pe 3:15

Machitidwe 15:26

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 13:50; 1Ak 15:30; 2Ak 11:23; Afi 2:29

Machitidwe 15:27

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1At 1:1; 1Pe 5:12
  • +Mac 16:4

Machitidwe 15:28

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yoh 16:13; Mac 5:32
  • +Mt 23:4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 54

    Nsanja ya Olonda,

    6/15/1990, tsa. 13

Machitidwe 15:29

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Ge 35:2; Eks 20:3; 34:15; Eze 20:30; 1Ak 8:1; 10:14
  • +Ge 9:4; Le 3:17; 7:26; 17:10; De 12:16, 23; 1Sa 14:32
  • +Le 17:13
  • +Ge 39:9; 1Ak 6:9; Aef 5:5; Akl 3:5; 1At 4:3; 1Pe 4:3
  • +Mac 21:25

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 39

    Mulungu Azikukondani, ptsa. 91-92

    Nsanja ya Olonda,

    12/15/2015, ptsa. 26-27

    6/15/2004, ptsa. 20-21, 29

    6/15/2000, tsa. 29

    1/15/1995, ptsa. 5-6

    6/15/1991, tsa. 9

    6/15/1990, tsa. 13

    6/1/1990, ptsa. 30-31

    3/1/1989, ptsa. 30-31

    5/1/1988, tsa. 17

    9/1/1986, tsa. 30

    3/15/1986, tsa. 15

    Zimene Baibulo Limaphunzitsa, ptsa. 139-140

    Baibulo Limaphunzitsa Chiyani, tsa. 130

    ‘Mulungu Apitirize Kukukondani’, tsa. 77

    Mwazi, ptsa. 4-5, 20, 22

    Galamukani!,

    6/8/1990, tsa. 6

    Kukhala ndi Moyo Kosatha, tsa. 216

    Kukambitsirana, ptsa. 313, 315

Machitidwe 15:30

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 11:26

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 54

Machitidwe 15:31

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Miy 15:30

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 54

Machitidwe 15:32

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 11:27; 13:1
  • +Mac 13:15; 18:23

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 114

Machitidwe 15:33

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 16:11

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 115

Machitidwe 15:34

Mawu a M'munsi

  • *

    Za mawu amene palibe, onani mawu a m’munsi pa Mt 17:21.

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 115

Machitidwe 15:35

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 13:1
  • +2Ak 11:7

Machitidwe 15:36

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2Ak 11:28

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 119

Machitidwe 15:37

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Akl 4:10; 2Ti 4:11

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 119-120

Machitidwe 15:38

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 13:13

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 120

    Nsanja ya Olonda,

    3/15/2010, tsa. 8

Machitidwe 15:39

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 4:36; 13:4
  • +Mac 11:20

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 120

    Nsanja ya Olonda,

    4/15/2011, tsa. 24

    3/15/2010, ptsa. 6, 8

    1/15/2003, ptsa. 19-20

    4/15/1998, ptsa. 22-23

    8/15/1993, ptsa. 21-22

    6/15/1990, ptsa. 13-14

    10/15/1989, tsa. 12

    Kukhala ndi Moyo Kosatha, ptsa. 233-234

Machitidwe 15:40

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 15:27
  • +Mac 14:26; Aef 3:7

Machitidwe 15:41

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 16:5

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Mac. 15:1Aga 2:12
Mac. 15:1Aga 5:2
Mac. 15:1Ge 17:10; Eks 12:48; Le 12:3
Mac. 15:2Mac 11:30; 16:4; Aga 2:1
Mac. 15:3Aro 15:24; 1Ak 16:6
Mac. 15:3Mac 13:4; 14:27
Mac. 15:3Mac 11:18
Mac. 15:4Mac 21:17
Mac. 15:4Mac 21:19
Mac. 15:5Mac 11:2
Mac. 15:5Eks 12:48
Mac. 15:6Miy 13:10; 15:22
Mac. 15:7Mko 9:16; Mac 15:2
Mac. 15:7Mac 10:34; 11:17
Mac. 15:81Mb 28:9; Yer 11:20; Mac 1:24
Mac. 15:8Mac 10:44; 11:15
Mac. 15:9Aga 3:28
Mac. 15:9Aga 2:16; 1Pe 1:22
Mac. 15:10Aga 5:1
Mac. 15:10Aga 3:10
Mac. 15:11Yes 53:11; Yoh 1:17; Aga 2:16
Mac. 15:11Mt 20:28
Mac. 15:12Aro 15:19
Mac. 15:13Mac 12:17
Mac. 15:14Mac 11:13; 2Pe 1:1
Mac. 15:14Yes 55:5; 1Pe 2:9
Mac. 15:16Amo 9:11
Mac. 15:17Amo 9:12
Mac. 15:18Yes 45:21
Mac. 15:19Mac 15:10
Mac. 15:20Ge 35:2; Eks 20:3; Eze 20:30; 1Ak 8:7; 10:14
Mac. 15:201Ak 6:9; Akl 3:5; 1At 4:3
Mac. 15:20Le 17:13
Mac. 15:20Ge 9:4; Le 3:17; 7:26; 17:10; 19:26; De 12:23; 15:23; 1Sa 14:32
Mac. 15:21Mac 13:15; 2Ak 3:15
Mac. 15:22Mac 1:23
Mac. 15:23Mac 11:26
Mac. 15:23Aga 1:21
Mac. 15:24Mac 15:1
Mac. 15:24Aga 2:4; Tit 1:10
Mac. 15:25Mac 1:14
Mac. 15:252Pe 3:15
Mac. 15:26Mac 13:50; 1Ak 15:30; 2Ak 11:23; Afi 2:29
Mac. 15:271At 1:1; 1Pe 5:12
Mac. 15:27Mac 16:4
Mac. 15:28Yoh 16:13; Mac 5:32
Mac. 15:28Mt 23:4
Mac. 15:29Ge 35:2; Eks 20:3; 34:15; Eze 20:30; 1Ak 8:1; 10:14
Mac. 15:29Ge 9:4; Le 3:17; 7:26; 17:10; De 12:16, 23; 1Sa 14:32
Mac. 15:29Le 17:13
Mac. 15:29Ge 39:9; 1Ak 6:9; Aef 5:5; Akl 3:5; 1At 4:3; 1Pe 4:3
Mac. 15:29Mac 21:25
Mac. 15:30Mac 11:26
Mac. 15:31Miy 15:30
Mac. 15:32Mac 11:27; 13:1
Mac. 15:32Mac 13:15; 18:23
Mac. 15:331Ak 16:11
Mac. 15:35Mac 13:1
Mac. 15:352Ak 11:7
Mac. 15:362Ak 11:28
Mac. 15:37Akl 4:10; 2Ti 4:11
Mac. 15:38Mac 13:13
Mac. 15:39Mac 4:36; 13:4
Mac. 15:39Mac 11:20
Mac. 15:40Mac 15:27
Mac. 15:40Mac 14:26; Aef 3:7
Mac. 15:41Mac 16:5
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano (nwt)
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
  • 15
  • 16
  • 17
  • 18
  • 19
  • 20
  • 21
  • 22
  • 23
  • 24
  • 25
  • 26
  • 27
  • 28
  • 29
  • 30
  • 31
  • 32
  • 33
  • 34
  • 35
  • 36
  • 37
  • 38
  • 39
  • 40
  • 41
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Machitidwe 15:1-41

Machitidwe

15 Ndiyeno amuna ena ochokera ku Yudeya+ anapita kumeneko ndi kuyamba kuphunzitsa abale kuti: “Mukapanda kudulidwa+ malinga ndi mwambo wa Mose,+ simungapulumuke.” 2 Koma Paulo ndi Baranaba sanamvane nawo ndipo anatsutsana nawo kwambiri. Choncho iwo anasankha Paulo ndi Baranaba, pamodzi ndi ena mwa iwo, kuti apite kwa atumwi ndi akulu ku Yerusalemu,+ kuti akawauze za kutsutsanako.

3 Tsopano mpingo utawaperekeza,+ amuna amenewa anapitiriza ulendo wawo kudzera ku Foinike ndi ku Samariya. Kumeneko anali kufotokoza mwatsatanetsatane za kutembenuka kwa anthu a mitundu ina,+ ndipo iwo anasangalatsa kwambiri abale onse.+ 4 Atafika ku Yerusalemu analandiridwa ndi manja awiri+ ndi mpingo, atumwi, komanso akulu. Kumeneko anafotokoza zinthu zambiri zimene Mulungu anachita kudzera mwa iwo.+ 5 Koma okhulupirira ena, amene kale anali m’gulu lampatuko la Afarisi anaimirira m’mipando yawo n’kunena kuti: “M’pofunika kuwadula+ ndi kuwalamula kuti azisunga chilamulo cha Mose.”+

6 Ndiyeno atumwi ndi akulu anasonkhana pamodzi kuti akambirane nkhani imeneyi.+ 7 Tsopano atatsutsana kwambiri,+ Petulo anaimirira, ndi kuwauza kuti: “Amuna inu, abale anga, mukudziwa bwino kuti m’masiku oyambirira Mulungu anandisankha ine pakati panu, kuti kudzera pakamwa panga, anthu a mitundu ina amve mawu a uthenga wabwino ndi kukhulupirira.+ 8 Ndipo Mulungu, amene amadziwa zamumtima,+ anachitira umboni mwa kuwapatsa mzimu woyera,+ monga anachitiranso kwa ife. 9 Ndipo iye sanasiyanitse m’pang’ono pomwe pakati pa ife ndi iwo.+ Koma anayeretsa mitima yawo chifukwa cha chikhulupiriro chawo.+ 10 Nanga tsopano n’chifukwa chiyani inu mukumuyesa Mulungu mwa kukanikizira goli pakhosi la ophunzira, goli+ limene makolo athu ngakhalenso ife sitinathe kulisenza?+ 11 Koma tsopano timakhulupirira kuti ife tidzapulumuka mwa kukoma mtima kwakukulu+ kwa Ambuye Yesu, mofanananso ndi anthu amenewa.”+

12 Pamenepo gulu lonselo linakhala chete, ndipo linayamba kumvetsera Baranaba ndi Paulo pamene anali kufotokoza zizindikiro ndi zodabwitsa zambiri zimene Mulungu anachita kudzera mwa iwo pakati pa anthu a mitundu ina.+ 13 Ataleka kulankhula, Yakobo anayankha kuti: “Amuna inu, abale anga, ndimvetsereni.+ 14 Sumeoni+ wafotokoza bwino mmene Mulungu anacheukira anthu a mitundu ina kwa nthawi yoyamba, kuti mwa iwo atengemo anthu odziwika ndi dzina lake.+ 15 Ndipo zimenezi zikugwirizana ndi mawu a m’Zolemba za aneneri. Mawuwo amati, 16 ‘Zimenezi zikadzatha ndidzabwerera ndi kumanganso nyumba ya Davide imene inagwa. Ndidzamanganso malo ogumuka a nyumbayo ndi kuiimikanso.+ 17 Ndidzachita zimenezi kuti anthu otsalirawo afunefune Yehova ndi mtima wonse. Amufunefune pamodzi ndi mitundu yonse ya anthu, anthu otchedwa ndi dzina langa, watero Yehova amene akuchita zinthu zimenezi,+ 18 zimene anatsimikiza kalekale kuti adzazichita.’+ 19 Choncho chigamulo changa n’chakuti, anthu amene akuchokera m’mitundu ina ndi kutembenukira kwa Mulungu, tisawavutitse.+ 20 Koma tiyeni tiwalembere kuti apewe zinthu zoipitsidwa ndi mafano,+ dama,*+ zopotola,+ ndi magazi.+ 21 Pakuti kuyambira kalekale, anthu akhala akulalikira mumzinda ndi mzinda mawu ochokera m’mabuku a Mose, chifukwa mabuku amenewa amawerengedwa mokweza m’masunagoge sabata lililonse.”+

22 Pamenepo atumwi ndi akulu pamodzi ndi mpingo wonse, anagwirizana zosankha amuna pakati pawo, kuti awatumize ku Antiokeya limodzi ndi Paulo ndi Baranaba. Choncho anasankha Yudasi wotchedwa Barasaba,+ ndi Sila, amuna otsogolera pakati pa abale. 23 Chotero ndi manja awo analemba kuti:

“Ife abale anu atumwi pamodzi ndi akulu, tikulembera inu abale athu ochokera mwa anthu a mitundu ina, okhala ku Antiokeya,+ ku Siriya ndi ku Kilikiya:+ Landirani moni! 24 Tamva kuti ena ochokera pakati pathu akhala akulankhula mawu okusautsani,+ pofuna kupotoza maganizo anu, ngakhale kuti ife sitinawapatse malangizo aliwonse.+ 25 Pa chifukwa chimenechi, tonse tagwirizana chimodzi,+ ndipo tavomerezana kuti tisankhe amuna oti tiwatumize kwa inu limodzi ndi okondedwa athu, Baranaba ndi Paulo.+ 26 Amenewa ndi amuna omwe apereka miyoyo yawo chifukwa cha dzina la Ambuye wathu Yesu Khristu.+ 27 Chotero tikutumiza Yudasi ndi Sila,+ kuti iwonso adzakufotokozereni zinthu zomwezi mwa mawu apakamwa.+ 28 Pakuti mzimu woyera+ pamodzi ndi ife taona kuti ndi bwino kuti tisakusenzetseni mtolo wolemera,+ kupatula zinthu zofunika zokhazi zomwe ndi 29 kupitiriza kupewa zinthu zoperekedwa nsembe kwa mafano,+ magazi,+ zopotola,+ ndi dama.+ Mukamapewa zinthu zimenezi mosamala kwambiri,+ zinthu zidzakuyenderani bwino. Tikukufunirani zabwino zonse!”

30 Amuna amenewa atanyamuka, analowera ku Antiokeya. Kumeneko anasonkhanitsa khamu lonse la anthu ndi kuwapatsa kalatayo.+ 31 Ataiwerenga, anakondwera chifukwa cha mawu olimbikitsawo.+ 32 Ndiponso popeza kuti Yudasi ndi Sila anali aneneri,+ analimbikitsa abalewo ndi mawu ambiri ndipo anawapatsa mphamvu.+ 33 Atakhala kumeneko kanthawi, abalewo anawalola kubwerera mumtendere+ kwa amene anawatuma. 34* —— 35 Koma Paulo ndi Baranaba anatsalira ku Antiokeya.+ Ndipo iwo pamodzi ndi enanso ambiri anali kuphunzitsa ndi kulengeza uthenga wabwino wa mawu a Yehova.+

36 Patapita masiku, Paulo anauza Baranaba kuti: “Tsopano, tiyeni tibwerere kumizinda yonse kumene tinafalitsa mawu a Yehova kuti tikachezere abale ndi kuwaona kuti ali bwanji.”+ 37 Chotero Baranaba anafunitsitsa kutenga Yohane, wotchedwa Maliko.+ 38 Koma Paulo anaona kuti n’kosayenera kumutenga kuti apite nawo. Anaona kuti n’kosayenera chifukwa ulendo wapita Yohane anawasiya ku Pamfuliya+ ndipo sanapite nawo ku ntchitoyi. 39 Pamenepo panabuka mkangano woopsa mpaka anapatukana. Baranaba+ anatenga Maliko ndipo anayenda ulendo wa pamadzi kulowera ku Kupuro.+ 40 Koma Paulo anasankha Sila,+ ndipo abale atamuikiza m’manja mwa Yehova kuti amusonyeze kukoma mtima kwakukulu, ananyamuka.+ 41 Iye anadzera ku Siriya ndi ku Kilikiya, ndipo anali kulimbitsa mipingo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena