Salimo 117 Tamandani Yehova, inu mitundu yonse ya anthu.+Mulemekezeni, inu anthu a mitundu yonse.*+ 2 Chifukwa chikondi chokhulupirika chimene amatisonyeza ndi chachikulu.+Kukhulupirika+ kwa Yehova kudzakhalapo mpaka kalekale.+ Tamandani Ya!*+