Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Chivumbulutso 8
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Zimene Zili Mʼbuku la Chivumbulutso

      • Anamatula chidindo cha 7 (1-6)

      • Kuliza malipenga 4 oyambirira (7-12)

      • Analengeza zokhudza masoka atatu (13)

Chivumbulutso 8:1

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 6:1
  • +Chv 5:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/2009, tsa. 32

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 129-131

Chivumbulutso 8:2

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 15:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    12/15/1988, tsa. 12

Chivumbulutso 8:3

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eks 30:1, 3
  • +Chv 5:8
  • +Chv 9:13

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 129-131

Chivumbulutso 8:4

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 141:2; Lu 1:10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 129-131

Chivumbulutso 8:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eks 19:16; Chv 4:5

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/2009, tsa. 32

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 131

Chivumbulutso 8:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 8:7, 8, 10, 12; 9:1, 13; 11:15

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 132

Chivumbulutso 8:7

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 16:2
  • +Eks 9:23-25; Sl 97:3, 5

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 133-134

    Nsanja ya Olonda,

    12/15/1988, tsa. 12

Chivumbulutso 8:8

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 17:12, 13; 57:20
  • +Eks 7:20

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 134-136

    Nsanja ya Olonda,

    12/15/1988, tsa. 12

Chivumbulutso 8:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 16:1, 3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 134-136

    Nsanja ya Olonda,

    12/15/1988, tsa. 12

Chivumbulutso 8:10

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 16:1, 4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 136-138

    Nsanja ya Olonda,

    12/15/1988, tsa. 12

Chivumbulutso 8:11

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Amo 5:7

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 136-139

    Nsanja ya Olonda,

    12/15/1988, tsa. 12

Chivumbulutso 8:12

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 16:1, 8
  • +Eks 10:22

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 138-141

    Nsanja ya Olonda,

    12/15/1988, tsa. 12

Chivumbulutso 8:13

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 9:12; 11:14
  • +Chv 8:2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 141

    Nsanja ya Olonda,

    4/1/1990, tsa. 31

    12/15/1988, tsa. 12

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Chiv. 8:1Chv 6:1
Chiv. 8:1Chv 5:1
Chiv. 8:2Chv 15:1
Chiv. 8:3Eks 30:1, 3
Chiv. 8:3Chv 5:8
Chiv. 8:3Chv 9:13
Chiv. 8:4Sl 141:2; Lu 1:10
Chiv. 8:5Eks 19:16; Chv 4:5
Chiv. 8:6Chv 8:7, 8, 10, 12; 9:1, 13; 11:15
Chiv. 8:7Chv 16:2
Chiv. 8:7Eks 9:23-25; Sl 97:3, 5
Chiv. 8:8Yes 17:12, 13; 57:20
Chiv. 8:8Eks 7:20
Chiv. 8:9Chv 16:1, 3
Chiv. 8:10Chv 16:1, 4
Chiv. 8:11Amo 5:7
Chiv. 8:12Chv 16:1, 8
Chiv. 8:12Eks 10:22
Chiv. 8:13Chv 9:12; 11:14
Chiv. 8:13Chv 8:2
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Chivumbulutso 8:1-13

Chivumbulutso Chimene Yohane Analandira

8 Atamatula+ chidindo cha 7,+ kumwamba sikunamveke phokoso lililonse kwa pafupifupi 30 minitsi. 2 Kenako ndinaona angelo 7+ amene amaimirira pamaso pa Mulungu, ndipo anapatsidwa malipenga 7.

3 Mngelo wina anafika atanyamula chiwiya chofukizira chagolide nʼkuima paguwa lansembe.+ Iye anapatsidwa zofukiza zambiri+ kuti azipereke nsembe limodzi ndi mapemphero a oyera onse paguwa lansembe lagolide,+ limene linali pamaso pa mpando wachifumu. 4 Utsi wa zofukizazo unakwera pamaso pa Mulungu kuchokera mʼdzanja la mngeloyo limodzi ndi mapemphero+ a oyera. 5 Koma nthawi yomweyo, mngeloyo anatenga chiwiya chofukizira chija nʼkudzazitsamo moto umene anapala paguwa lansembe nʼkuuponyera padziko lapansi. Ndiyeno kunagunda mabingu, kunamveka mawu, kunachita mphezi+ komanso chivomerezi. 6 Angelo 7 amene anali ndi malipenga 7 aja, anakonzekera kuliza malipengawo.+

7 Mngelo woyamba analiza lipenga lake. Atatero, panaoneka matalala ndi moto zosakanikirana ndi magazi ndipo zinaponyedwa padziko lapansi.+ Gawo limodzi mwa magawo atatu a dziko lapansi linapsa, gawo limodzi mwa magawo atatu a mitengo linapsa komanso zomera zonse zobiriwira zinapsa.+

8 Mngelo wachiwiri analiza lipenga lake. Ndipo chinachake chokhala ngati phiri lalikulu limene likuyaka moto chinaponyedwa mʼnyanja.+ Zitatero gawo limodzi mwa magawo atatu a nyanja, linasanduka magazi.+ 9 Ndipo gawo limodzi mwa magawo atatu a zamoyo zamʼnyanja zinafa.+ Komanso gawo limodzi mwa magawo atatu a ngalawa, linasweka.

10 Mngelo wachitatu analiza lipenga lake. Ndipo nyenyezi yaikulu imene inkayaka ngati nyale inagwa kuchokera kumwamba. Inagwera pagawo limodzi mwa magawo atatu a mitsinje, ndi pa akasupe a madzi.+ 11 Dzina la nyenyeziyo ndi Chitsamba Chowawa. Choncho gawo limodzi mwa magawo atatu a madzi linakhala lowawa ndipo anthu ambiri anafa ndi madziwo chifukwa anali owawa.+

12 Mngelo wa 4 analiza lipenga lake. Atatero, gawo limodzi mwa magawo atatu a dzuwa linamenyedwa.+ Komanso gawo limodzi mwa magawo atatu a mwezi ndi a nyenyezi linamenyedwa. Zinatero kuti gawo limodzi mwa magawo atatu a zinthu zimenezi lichite mdima,+ komanso kuti gawo limodzi mwa magawo atatu a usana lisalandire kuunika, chimodzimodzinso usiku.

13 Ndiyeno ndinaona chiwombankhanga chikuuluka pafupi mumlengalenga ndipo ndinamva chikulankhula ndi mawu okweza akuti: “Tsoka, tsoka, tsoka+ kwa amene akukhala padziko lapansi, chifukwa cha kulira kwa malipenga otsalawo, amene angelo atatu atsala pangʼono kuwaliza!”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena