Genesis 8:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Masiku onse amene dziko lapansi lidzakhalapo, kubzala mbewu ndi kukolola sikudzatha. Ndiponso, nyengo yozizira ndi yotentha, chilimwe ndi chisanu, usana ndi usiku, zidzakhalapobe.”+ Yesaya 55:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti monga momwe mvula ndi chipale chofewa zimagwera kuchokera kumwamba, osabwereranso kumeneko mpaka zitanyowetsa kwambiri nthaka n’kumeretsa zomera ndi kuzibereketsa,+ wobzala mbewu n’kupatsidwa zokolola komanso wakudya n’kupatsidwa chakudya,+ 2 Akorinto 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano amene amapereka mbewu kwa wobzala, amenenso amapereka chakudya kuti anthu adye,+ adzakupatsani mbewu zoti mubzale ndipo adzakupatsani zimenezi mowolowa manja. Adzawonjezeranso zipatso za chilungamo chanu.)+
22 Masiku onse amene dziko lapansi lidzakhalapo, kubzala mbewu ndi kukolola sikudzatha. Ndiponso, nyengo yozizira ndi yotentha, chilimwe ndi chisanu, usana ndi usiku, zidzakhalapobe.”+
10 Pakuti monga momwe mvula ndi chipale chofewa zimagwera kuchokera kumwamba, osabwereranso kumeneko mpaka zitanyowetsa kwambiri nthaka n’kumeretsa zomera ndi kuzibereketsa,+ wobzala mbewu n’kupatsidwa zokolola komanso wakudya n’kupatsidwa chakudya,+
10 Tsopano amene amapereka mbewu kwa wobzala, amenenso amapereka chakudya kuti anthu adye,+ adzakupatsani mbewu zoti mubzale ndipo adzakupatsani zimenezi mowolowa manja. Adzawonjezeranso zipatso za chilungamo chanu.)+