Genesis 19:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma Loti anawaumiriza kwambiri+ moti mpaka iwo anapita naye kunyumba kwake. Kumeneko anawakonzera phwando,+ n’kuwaphikira mikate yopanda chofufumitsa,+ ndipo anadya. 2 Mafumu 6:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Chotero mfumuyo inawakonzera phwando lalikulu ndipo anayamba kudya ndi kumwa. Atatha anawauza kuti azipita ndipo anapita kwa mbuye wawo. Kuchokera pamenepo, magulu a achifwamba+ a Asiriya sanabwerenso ku Isiraeli.
3 Koma Loti anawaumiriza kwambiri+ moti mpaka iwo anapita naye kunyumba kwake. Kumeneko anawakonzera phwando,+ n’kuwaphikira mikate yopanda chofufumitsa,+ ndipo anadya.
23 Chotero mfumuyo inawakonzera phwando lalikulu ndipo anayamba kudya ndi kumwa. Atatha anawauza kuti azipita ndipo anapita kwa mbuye wawo. Kuchokera pamenepo, magulu a achifwamba+ a Asiriya sanabwerenso ku Isiraeli.