Yoswa 24:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Isaki anabereka Yakobo ndi Esau.+ Pambuyo pake Esau ndinam’patsa phiri la Seiri kuti likhale lake.+ Kenako, Yakobo ndi ana ake anapita ku Iguputo.+ Aheberi 11:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mwa chikhulupiriro, Isaki nayenso anadalitsa Yakobo+ ndi Esau,+ pa nkhani yokhudza zinthu zimene zinali kubwera.
4 Isaki anabereka Yakobo ndi Esau.+ Pambuyo pake Esau ndinam’patsa phiri la Seiri kuti likhale lake.+ Kenako, Yakobo ndi ana ake anapita ku Iguputo.+
20 Mwa chikhulupiriro, Isaki nayenso anadalitsa Yakobo+ ndi Esau,+ pa nkhani yokhudza zinthu zimene zinali kubwera.