Genesis 27:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Choncho anamuyandikira ndi kum’psompsona, ndipo anatha kumva kafungo ka zovala zake.+ Pamenepo anamudalitsa kuti: “Eya, kafungo ka mwana wanga kakununkhira ngati fungo lokoma la munda umene Yehova waudalitsa.
27 Choncho anamuyandikira ndi kum’psompsona, ndipo anatha kumva kafungo ka zovala zake.+ Pamenepo anamudalitsa kuti: “Eya, kafungo ka mwana wanga kakununkhira ngati fungo lokoma la munda umene Yehova waudalitsa.